Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 13:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu, pakuika maliro a munthu wina, anaona gulu la nkhondo, naponya mtembo m'manda mwa Elisa; koma pamene mtembowo unakhudza mafupa a Elisa, wakufayo anauka, naima ciriri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 13

Onani 2 Mafumu 13:21 nkhani