Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 13:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati, Tsegulani zenera la kum'mawa. Nalitsegula. Nati Elisa, Ponyani. Naponya. Nati iye, Mubvi wa cipulumutso wa Yehova ndiwo mubvi wa kukupulumutsani kwa Aaramu; popeza mudzakantha Aaramu m'Afeki mpaka mudzawatha.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 13

Onani 2 Mafumu 13:17 nkhani