Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 12:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehoyada wansembe anatenga bokosi, naboola ciboo pa cibvundikilo cace, naliika pafupi pa guwa la nsembe, ku dzanja lamanja polowera nyumba ya Yehova; ndipo ansembe akusunga pakhomo anaikamo ndarama zonse anabwera nazo anthu ku nyumba ya Yehova,

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 12

Onani 2 Mafumu 12:9 nkhani