Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 12:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma sanapangira nyumba ya Yehova mbale zasiliva, mbano, mbale zowazira, malipenga, zotengera ziri zonse zagolidi, kapena zotengera ziri zonse zasiliva, kuzipanga ndi ndarama adabwera nazo ku nyumba ya Yehova;

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 12

Onani 2 Mafumu 12:13 nkhani