Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 11:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atsogoleri a mazana anacita monga mwa zonse anawalamulira Yehoyada wansembe, natenga yense anthu ace olowera pa Sabata, ndi oturukira pa Sabata, nafika kwa Yehoyada wansembeyo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 11

Onani 2 Mafumu 11:9 nkhani