Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 11:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Napita nao atsogoleri a mazana, ndi opha anthu, ndi otumikira, ndi anthu onse a m'dziko; ndipo iwo anatsika nayo mfumu ku nyumba ya Yehova, nadzera njira ya cipata ca otumikira, kumka ku nyumba ya mfomu. Nakhala Iye pa cimpando ca mafumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 11

Onani 2 Mafumu 11:19 nkhani