Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 11:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehoyada anacita cipangano pakati pa Yehova ndi mfomu ndi anthu, akhale anthu a Yehova; pakati pa mfumunso ndi anthu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 11

Onani 2 Mafumu 11:17 nkhani