Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 11:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atatero, anaturutsa mwana wa mfumu, namuika korona, nampatsa buku la umboni, namlonga ufumu, namdzoza, naomba m'manja, nati, Mfomu ikhale ndi movo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 11

Onani 2 Mafumu 11:12 nkhani