Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 10:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Yehu, Popeza wacita bwino, pocita coongoka pamaso panga, ndi kucitira nyumba ya Ahabu monga mwa zonse zinali m'mtima mwanga, ana ako a ku mbadwo wacinai adzakhala pa mpando wacifumu wa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:30 nkhani