Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 10:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mundiitanire tsono adze kwa ine aneneri onse a Baala, ompembedza onse, ndi ansembe ace onse, asasowe mmodzi; pakuti ndiri nayo nsembe yaikuru yocitira Baala; ali yense wosapenyekapo sadzakhala ndi moyo. Kama Yehu anacicita monyenga, kuti akaononge otumikira Baala.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:19 nkhani