Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 10:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atacoka pamenepo, anakomana naye Yehonadabu mwana wa Rekabu wakudzamcingamira; namlankhula, nanena naye, Mtima wako ngwoongoka kodi, monga mtima wanga ubvomerezana nao mtima wako? Nati Yehonadabu, Momwemo. Ukatero undipatse dzanja lako. Nampatsa dzanja lace, namkweretsa pali iye pagareta.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:15 nkhani