Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 1:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anabwereza kutuma kwa iye mtsogoleri wina ndi makumi asanu ace. Ndipo iye anayankha nanena naye, Munthu wa Mulungu iwe, itero mfumu, Tsika msanga.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 1

Onani 2 Mafumu 1:11 nkhani