Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 9:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapyola dziko lamapiri la Efraimu, napyola dziko la Salisa, koma sanawapeza; pamenepo anapyolanso dziko la Salimu; koma panalibe pamenepo, napyola dziko la Abenjamini, osawapeza.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:4 nkhani