Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 9:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wophikayo ananyamula mwendo ndi mnofu wace, nauika pamaso pa Sauli. Ndipo Samueli anati, Onani cimene tinakuikirani muciike pamaso panu, nudye; pakuti ici anakuikirani kufikira nthawi yonenedwa, popeza ndinati, Ndinaitana anthuwoo Comweco Sauli anadya ndi Samueli tsiku lija.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:24 nkhani