Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 9:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mawa, monga dzuwa lino, ndidzakutumizira munthu wocokera ku dziko la Benjamini, udzamdzoza iye akhale mtsogoleri wa anthu anga Israyeli, kuti akawapulumutse anthu anga m'manja a Afilisti; pakuti Ine ndinapenya pa anthu anga, popeza kulira kwao kunandifika Ine.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:16 nkhani