Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 8:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Samueli, Umvere mau ao, nuwalongere mfumu, Ndipo Samueli anati kwa amuna a Israyeli, Mupite, munthu yense ku mudziwace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 8

Onani 1 Samueli 8:22 nkhani