Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 8:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo idzatenga limodzi la magawo khumi la mbeu zanu, ndi la minda yanu yamphesa, nidzalipatsa akapitao ace, ndi anyamata ace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 8

Onani 1 Samueli 8:15 nkhani