Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 7:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Samueli anatenga mwala nauimika pakati pa Mizipa ndi Seni, naucha dzina lace. Ebenezeri, nati, Kufikira pano Yehovaanatithandiza.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 7

Onani 1 Samueli 7:12 nkhani