Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 7:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu a ku Kiriati-yearimu anabwera, natenga likasa la Yehova, nafika nalo m'nyumba ya Abinadabu paphiri; napatula mwana wace wamwamuna Eleazeri kuti asunge likasa la Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 7

Onani 1 Samueli 7:1 nkhani