Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 6:20-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Ndipo a ku Betisemesi anati, Akhoza ndani kuima pamaso pa Yehova, Mulungu Woyera uyu? Ndipo adzakwera kwa yani pakuticokera ife?

21. Ndipo anatumiza mithenga kwa anthu a ku Kiriati-yearimu, nati, Afilisti anabwera nalo likasa la Yehova, mutsike; ndi kukwera nalo kwanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 6