Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anthu a ku Asidodi anaona kuti ncomweco, anati iwowa, Likasa la Mulungu wa Israyeli lisakhalitse ndi ife; popeza dzanja lace litiwawira ife, ndi Dagoni mulungu wathu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 5

Onani 1 Samueli 5:7 nkhani