Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 5:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mawa mwace polawirira, taonani, Dagoni adagwa pansi, nagona cafufumimba patsogolo pa likasa la Yehova; ndipo mutu wace ndi zikhato zonse ziwiri za manja ace zinagona zoduka paciundo; Dagoni anatsala thupi lokha.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 5

Onani 1 Samueli 5:4 nkhani