Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 4:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Afilistiwo pakumva kubuma pa kupfuula kwao, anati, Phokoso ili la kupfuula kwakukuru ku zithando za Aisrayeli litani? Ndipo anamva kuti likasa la Yehova lidzafika ku zithandozo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:6 nkhani