Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 4:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anamucha dzina la mwanayo Ikabodi, nati, Ulemerero wacoka kwa Israyeli; cifukwa likasa la Mulungu linalandidwa, ndi cifukwa ca mpongozi wace ndi mwamuna wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:21 nkhani