Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 30:30-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. ndi kwa iwo a ku Horima, ndi kwa iwo a ku Korasani, ndi kwa iwo a ku Ataki;

31. ndi kwa iwo a ku Hebroni, ndi kumalo konse kumene Davide ndi anthu ace adafoyendayenda.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 30