Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 3:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anabwereza kumuitana, ndi kuti, Samueli. Ndipo Samueli anauka, napita kwa Eli, nati, Ndine, pakuti mwandiitana ndithu. Koma iye anayankha, Sindinaitana, mwana wanga; kagone.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 3

Onani 1 Samueli 3:6 nkhani