Ndipo Aisrayeli onse, kuyambira ku Dani kufikira ku Beereseba anazindikira kuti Samueli anakhazikika akhale mneneri wa Yehova.