Ndipo Yehova ananena ndi Samueli, Taona, ndidzacita mwa Israyeli coliritsa mwini khutu kwa munthu yense wakucimva.