Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 29:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Akisi anaitana Davide, nanena naye, Pali Yehova, wakhala woongoka mtima, ndipo kuturuka kwako ndi kubwera kwako pamodzi ndi ine m'gulumo kundikomera; pakuti sindinaona coipa mwa iwe kuyambira tsiku la kufika kwako kufikira lero; koma akalongawo sakukomera mtima.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 29

Onani 1 Samueli 29:6 nkhani