Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 29:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco Davide analawirira, iye ndi anthu ace, kuti amuke m'mawa ndi kubwera ku dziko la Afilisti. Ndipo Afilisti anakwera ku Jezreeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 29

Onani 1 Samueli 29:11 nkhani