Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 27:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ndi anthu ace anakwera, nathira nkhondo yobvumbulukira pa Agesuri, ndi Agirezi, ndi Aamaleki; pakuti awa ndiwo anthu akale a m'dziko lija, njira ya ku Suri kufikira ku dziko la Aigupto.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 27

Onani 1 Samueli 27:8 nkhani