Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 27:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anati kwa Akisi, Ngati mwandikomera mtima, andipatse malo kumudzi kwina kumiraga, kuti ndikakhale kumeneko; pakuti mnyamata wanu adzakhala bwanji m'mudzi wacifumu pamodzi ndi inu?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 27

Onani 1 Samueli 27:5 nkhani