Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 26:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace mbuye wanga mfumu amvere mau a kapolo wace. Ngati ndi Yehova anakuutsirani inu kutsutsana ndi ine, alandire copereka; koma ngati ndi ana a anthu, atembereredwe pamaso pa Yehova, pakuti anandipitikitsa lero kuti ndisalandireko colowa ca Yehova, ndi kuti, Muka, utumikire milungu yina.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 26

Onani 1 Samueli 26:19 nkhani