Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 26:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Azifi anafika kwa Sauli ku Gibeya, nati, Kodi Davide sali kubisala m'phiri la Hagila, kupenya kucipululu!

2. Ndipo Sauli ananyamuka, natsikira ku cipululu ca Zifi, ndi anthu zikwi zitatu a Israyeli osankhika, kukafuna Davide m'cipululu ca Zifi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 26