Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 25:43-44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

43. Davide anatenganso Ahinoamu wa ku Yezreeli, ndipo onse awiri anakhala akazi ace.

44. Pakuti Sauli anapatsa Mikala, mwana wace, mkazi wa Davide, kwa Paliti mwana wa Loisi, wa ku Galimu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25