Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 25:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo, kudalitsike kucenjera kwako, nudalitsike iwe, pakuti unandiletsa kusakhetsa mwazi, ndi kusabwezera cilango ndi dzanja la ine ndekha.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:33 nkhani