Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 25:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atagwadira pa mapazi ace anati, Pa ine, mbuye wanga, pa ine pakhale ucimowo; ndipo mulole mdzakazi wanu alankhule m'makutu anu, nimumvere mau a mdzakazi wanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:24 nkhani