Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 24:21-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Cifukwa cace tsono undilumbirire ndi Yehova, kuti sudzatha mbeu yanga nditamuka ine, ndi kuti sudzaononga dzina langa m'nyumba ya atate wanga.

22. Ndipo Davide analumbirira Sauli. Sauli namuka kwao; koma Davide ndi anthu ace anakwera kumka kungaka.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 24