Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 23:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anadziwa kuti Sauli analikulingalira zomcitira zoipa; nati kwa Abyatara wansembe, Bwera kuno ndi efodi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:9 nkhani