Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 23:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukanitu kuti mukadziwitse ndithu, ndi kudziwa ndi kuona mbuto m'mene akhalitsa, ndi amene adamuona m'menemo; cifukwa anandiuza kuti iye acita mocenjera ndithu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:22 nkhani