Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 23:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Davide anafunsira kwa Yehova, nati, Ndimuke kodi kukakantha Afilisti aja? Ndipo Yehova anati kwa Davide, Muka, nukanthe Afilisti, ndi kupulumutsa Keila.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:2 nkhani