Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 23:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo a ku Zifi anakwera kwa Sauli ku Gibeya, nati, Davide salikubisala kwathu kodi, m'ngaka za m'nkhalango, m'phiri la Hakila. Umene Uri kumwera kwa cipululu?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:19 nkhani