Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 21:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ananena ndi Ahimeleki, Nanga pano m'dzanja mwanu mulibe mkondo kapena lupanga kodi? cifukwa ine sindinatenge lupanga langa kapena zida zanga, popeza mrandu wa mfumu ukuti ndifulumire.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 21

Onani 1 Samueli 21:8 nkhani