Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 21:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anafika ku Nobi kwa! Ahimeleki wansembeyo; ndipo Ahimeleki anadza kukomana ndi Davide alikunjenjemera, nanena naye, Muli nokha bwanji, palibe munthu wina nanu?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 21

Onani 1 Samueli 21:1 nkhani