Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 20:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Jonatani anapfuulira mnyamatayo, nati, Yendesa, fulumira, usaima. Ndi mnyamata wa Jonatani anatola mibvi, nafika kwa mbuye wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:38 nkhani