Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 20:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Sauli anapsa mtima ndi Jonatani, nanena naye, Iwe mwana wa mkazi wa matsutso ndi wopikisana, sindidziwa kodi kuti wasankha mwana wa Jeseyo kudzinyaza wekha, ndi usiwa wa mai wako yemwe?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:30 nkhani