Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 20:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taona, ndidzatumiza mnyamatayo, ndi kuti, Kafune mibviyo, Ndikamuuza mwanayo, kuti, Taona mibvi iri cakuno; uitole nubwere, popeza pali mtendere kwa iwe, palibe kanthu, pali Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 20

Onani 1 Samueli 20:21 nkhani