Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 2:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akacimwira munthu mnzace oweruza adzaweruza mrandu wace; koma ngati munthu acimwira Yehova, adzampembedzera ndani? Koma ngakhale adatero, iwo aja anakhalabe osamvera mau a atate wao, cifukwa Yehova adati adzawaononga.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:25 nkhani