Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 19:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli anatumiza mithenga ku nyumba ya Davide imdikire, ndi kumupha m'mawa; koma Mikala mkazi wa Davide anamuuza, nati, Ukapanda kupulumutsa moyo wako usiku uno, udzaphedwa ndithu m'mawa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 19

Onani 1 Samueli 19:11 nkhani