Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 18:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo mafumu a Afilisti anaturuka; ndipo nthawi zonse anaturuka iwo, Davide anali wocenjera koposa anyamata onse a Sauli, comweco dzina lace linatamidwa kwambiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 18

Onani 1 Samueli 18:30 nkhani